Seed meets good planting rains

Throughout Malawi farmers have been receiving good planting rains and seeds are coming to life nicely.

A new life of a good food crop starts with the seed. The past few months the Demeter Seed team have worked hard on getting Demeter seed of maize and legumes to over 900 agro outlets spread out accross Malawi. This has given the farmers access to the vital input they need for a successful food crop – Demeter seed.

to the farmer

Alimi ku Malawi akonzekera mvula

Malawi farmers prepared for the rains.

Ndi nyengo ya mvula yomwe ili pafupi alimi mdziko lonse la Malawi asosa kale minda yawo kuyembekezera kudzala mbeu. Demeter seed company yapereka kale mbeu mmasitolo osiyanasiyana oposela 900 mdziko lonse la Malawi kuti mlimi ayipeze mosavutikira ndi mdera lomwe akukhala.

Ndi sosa komanso mbeu zomwe zafika kale mmadera osiyanasiyana chiyembekezo cholandira mvula yabwino chilipo

With the rainy season approaching farmers throughout Malawi have prepared their lands for planting. The Demeter Seed company has made available seeds through over 900 outlets nationwide serving the farmer close to his home.

With lands prepared and inputs in place the rains can come and hopefully plentiful.

IMG-20181115-WA0014.jpg

 

 

 

Kasinthasintha wa ulimi wa Mtedza ndi chimanga umabweretsa zokolora zochuluka

Groundnut planting with maize for better yields

Mukadzala mosinthanasinthana mbeu ya Mtedza ndi chimanga zimathandizila kukolola zochuluka pa mbeu zonse ziwirizi. Mtedza umagwiritsa ntchito chonde chotsalila mmunda mmene munali chimanga ndiponso umakozanso nthaka yomwe imapindulira chimanga / Groundnuts planted in rotation with maize improve the productivity of both crops. Groundnuts make good use of leftover nutrients while improving soil conditions for following maize crop.

Demeter seed yagawa kale mbeu ya Mtedza wa CG7  ndiponso ikupititiza kutero mmasitolo onse a Farmers World,  Agora ndi ma agrodealers osiyanasiyanasiyana mmadera onse omwe mumalimidwa Mtedza muno MMalawi / Demeter Seed is distributing seed of the groundnut variety CG7 to branches of Farmers World and AGORA as well as various agro-dealers in groundnut producing areas in Malawi.

Click here for more information on groundnut production.

 

 

6 things agroecology can do for farming and the environment

Agroecology has returned to the global spotlight, as one approach to bring farmers closer to meeting challenges [like rising food demand]. Agroecology emerged as a science which supports food security and sustainable agriculture. In the 1960s, it was studied as the interaction between crops and the environment …. Promoting farming systems that are beneficial to producers and society, as well as the earth’s ecosystems has become a central theme ….

Read more >>

 

Farmers happy with Demeter Seed carry bag

Alimi MMALAWI akusankha mbeu za Demeter kamba ka kudalilika Kwake ndi kaberekedwe kake kochuluka mmadera osiyanasiyana. Mmadera ena alimi ambiri akusangalala kamba kolandilanso zikwama za Demeter zomwe akumanyamulira mbeu zawo.

Farmers in Malawi choose Demeter seed for good performance in the field and reliable food production. At selected distribution points they are especially happy with the carry bag they get to transport the seed back home.

img-20181029-wa0003

Alimi akusankha mbeu za Demeter mu ndondomeko ya Subsidy / Farmers choose Demeter seed for coupons

Pamene makuponi a mbeu zotsika mtengo ayamba, alimi ambiri akusankha mbeu za Demeter mmadera osiyanasiyana muno MMalawi.

Demeter seed yawonetsa ukadaulo ndi kudalilika popanga mbeu zodzetsa chakudya chambiri ndi zodalilika zomwe alimi amayembekezera.

Farmers throughout Malawi are looking for value for their coupons and choose Demeter seed.

Demeter seed has proven to be reliable to produce a food crop farmers are aiming for.

Blog at WordPress.com.

Up ↑