Cowpeas

Cowpeas

Cowpea

COWPEA PRODUCTION GUIDE

 • Prepare land very early before November,  to plant your seed with the first soaking rains.
 • Space your ridges at 75 – 90cm apart. Plant 2seed per station spaced at 20 cm apart. Seed need around 20kg/ha or 8kg/acre.
 • Cowpeas does well even without fertilizers, however, application of 50kg of 23:21:0 +4S per acre is advantageous.
 • Crop be kept weed free at all times, especially the very first five weeks from time of planting.
 • Cowpeas is very susceptible to pest attack more especially during flowering, therefore periodic sprays of carbaryl at a rate of 85g to 14 litres of water is recommended.
 • Harvest your pods as soon as they start drying and sun dry to complete drying process.
 • Threshing be done by hand or use small sticks to avoid breaking seed.
 • Treat thoroughly dried seed with actellic super at a rate of 25g to a 50kg bag.
 • Store your seed in a cool dry place that has no leakage.

NOTE:     Also seek technical advise from the agricultural extension staff of your area.

KABZALIDWE KA MBEWU YA KHOBWE

 • Konzani munda wanu moyambilira usanafike mwezi wa November, kuti mubzale mbewu yanu ndi mvula yoyambilira.
 • Konzani mizere yotalikirana 75 kapena 90 cms. Ndipo bzalani mbewu ziwiri paphado.
 • Khobwe amachita bwino ngakhale osathira feteleza, komano dzaonetsa kuti kuthira thumba limodzi la feteleza wa chitowe (23:21:0 + 4S ) pa ekala, kwaonetsa phindu lalikuru kumakololedwe.
 • Onetsetsani kuti mbewu yanu mulibe udzu makamaka masabata asanu oyambilira.
 • Tizilombo tambiri timakonda mukhobwe, tsono mpofunika kumapopera mankhwala a seveni (carbaryl) pamene tizilombo tiwoneka mu mbewu zanu.
 • Chotsani khobwe amene akuonetsa kuwuma ndipo pitilizani kumuyanika kuti awume bwino.
 • Sendani ndi manja kapena pogwiritsa timitengo tatingono kuwopela kutswanya khobwe.
 • Sungani mbewu yanu mumatumba abwino ndipo thirani mankhwala otetezera ku anakafumbwe. 25g za actellic super ndiokwanila thumba lolemera 50kg.
 • Sungani mbewu pamalo odzidzilirapo koma owuma.

CHIDZIWITSO:        Funsirani zoonjezera kuchokera kwa alangizi a mdera lanu.

Create a free website or blog at WordPress.com.

Up ↑

%d bloggers like this: