Maize

GS DAL product info Maize


MAIZE PRODUCTION GUIDE

 • Clear the land as early as possible before November for summer crop.
 • Make ridges or rows at 60 – 75cm.
 • Plant one seed per station, spaced at 25 – 30cm. Seed need around 25kg/ha or 10kg/acre.
 • Apply 100 kg basal fertilizer, preferably 23:21:0 + 4s at 5gms/plant just after emergency.
 • Keep the field weed free all the time.
 • Apply top- dressing fertilizer like urea, when plants are 30cm high or 21 days after emergency. About 9 gr per plant.
 • Harvest when the crop is at 18% moisture content and leave it to dry in granaries.
 • Shell and bag when the crop is at 12.5% moisture content. Remember to treat with pesticide to avoid weavil.

NOTE:     Also seek technical advise from the agricultural extension staff of your area.

Click here for info on Fall Armyworm

KALIMIDWE KA MBEWU 

 • Sosani ndi kugalauza munda wanu moyambilira usanafike mwedzi wa November.
 • Konzani mizere motalikira ma sentimita osachepera 60 koma osadutsa 75cm.
 • Bzalani mbewu imodzi pa phando, koma mosatalikirana mochepera ma sentimita 25 komanso osadutsa 30cm.
 • Thilani feteleza wa chitowe pogwiritsa ntchito chitsekero cha fanta (5gms) pa phando liri onse..
 • Palilani munda wanu ndikuonetsetsa kuti mulibe udzu nthawi yina ili yonse.
 • Feteleza wobeleketsa athilidwe pasanathe masabata atatu (21 days) chimelereni cha mbewu yanu. About 9 gr per plant.
 • Kololani pamene makwawule awuma.
 • Tonolani chimanga chanu pomwe mtima wa chimanga wauma, ndipo ikani mmatumba. Kumbukirani kuthila mankhwala olimbana ndi a nankafumbwe.

CHIDZIWITSO:        Funsirani zoonjezera kuchokera kwa alangizi a mdera lanu.

 

Create a free website or blog at WordPress.com.

Up ↑

%d bloggers like this: