Soyabeans

Soyabeans

Soyabean Tikolore Early maturity 90 days 2.5(50x50kg/ha) Resistent to soyabean rust

Performance TIKOLORE in Malawi national soyabean trials 2017/2018

SOYABEAN PRODUCTION GUIDE

 • Prepare land early before the month of November.
 • Space your ridges from 75 – 90 cm. and plant 1 seed per station spaced at 5-10cm. Make 2rows on a ridge. Seed need around 80kg/ha or 32kg/acre.
 • Ensure to plant seed that has been inoculated with appropriate rhizobium.
 • It has shown that application of 100kgs/acre of 23:21:0 +4S has yield advantage.
 • Keep the field free from weeds, especially the first 5 – 8weeks from planting.
 • Harvest when most of the pods are thoroughly dry, uproot and sun dry the stems holding pods. When dry enough, start threshing by use of thinner sticks. Up-rooting must be done in the early hours to avoid shattering of seed.
 • Store your seed in a cool dry place that does not leak.

NOTE:     Also seek technical advise from the agricultural extension staff of your area.

KALIMIDWE KA MBEWU YA MDZADZA NKHOKWE YA NYEMBA ZA SOYA.

 • Sosani ndi kugalauza munda usanakwane mwedzi wa November.
 • Konzani midzere motalikirana kwa pakati pa 75 -90cm. Bzalani mbewu iimodzi pa dzenje ndipo maenje atalikirane pa mpata wa pakati pa 5- 10cm. Ndipo pa mzere pakhala mikwasa iwiri.
 • Onetsetsani kuti mbewu yasakanizidwa ndi mankhwala a inokulamu. (feteleza wa munthaka)
 • Kwaonetsa kuti pamakhala phindu ngati muthira feteleza wa chitowe (23:21:0 + 4S ) wolemera 100kg/acre.
 • Onetsetsani kuti mmunda mwanu musakhale tchire pa nthawi yina iri yonse, makamaka sabata zoyambilira zisanu ndi chimodzi kapena masabata asanu ndi atatu.
 • Yambani kudzula soya wanu pamene waonetsa kuwuma kwa nyemba ndiponso kuyoyoka kwa masamba. Tchito yodzula soya idzichitika mmawa dzuwa lisanatenthe kwambiri kuwopera kothetheka kwa nyemba.
 • Menyani soya ndi timitengo tatingono powopera kutswanya mbewu.
 • Sungani mbewu mu matumba atsopano ndipo mmalo owuna koma odzidzilirako, mosadontha.

CHIDZIWITSO:        Funsirani zoonjezera kuchokera kwa alangizi a mdera lanu.

Report on USAID/Feed the Future soyabean Pan African oyabean testing

Blog at WordPress.com.

Up ↑

%d bloggers like this: