Mbeu ya soya ya mtundu wa Tikolore kuchokera ku Demeter ikuchita bwino mminda yonse ya zionetsero muno M’MALAWI

Mbeu ya soya ya mtundu wa Tikolore kuchokera ku Demeter ikuchita bwino mminda yonse ya zionetsero muno M’MALAWI/Demeter soyabean high yielding in in Malawi trials

Soyabeans

Soyabean Tikolore Early maturity 90 days 2.5(50x50kg/ha) Resistent to soyabean rust

Performance TIKOLORE in Malawi national soyabean trials 2017/2018

Demeter seed ikuthandiza alimi kukonzekera kubyala mbeu

Demeter seed ikuthandiza alimi kukonzekera kubyala mbeu. / Demeter Seed helping Malawi farmers get ready.

Demeter ikupitiriza kutumiza mbeu mmadera osiyanasiyana muno MMalawi ndipo tatumiza kale 900mt kuti alimi apeze mbewu mosavutikira. / To enable farmers to be well prepared for planting when the rains come, Demeter Seed is dispatching seed to close to 900 agro-input shops countrywide.

Mbeu za mgulu la nyemba komanso masamba zikupezeka mmilingo yosiyanasiyana komanso mitundu ingapo. / Seed of maize, legumes and vegetables will be available for various varieties and in selected pack sizes.

Mu ndondomeko ya Fisp Demeter ikupatsirani mbeu ya chimanga mu mlingo wa 5 kilogalamu, monga: / For the government  FISP program Demeter Seed is sending out stocks of the following:

Chimanga / Maize (in 5kg bags)

  • Mchotsa Nkhawa (ZM523) – yocha mwapakatikati /medium season
  • Kachamsanga (ZM309) – yocha mofulumila / early
  • Mphangala (MH26) – ya hybrid, yocha mwapakatikati  / medium season & hybrid yield

Demeter ikupezekanso ndi mbeu za mgulu la nyemba monga: / Demeter has the following range of legume seed: (in 1 kg bags)

  • Nyemba za – CHUMA / Sugarbeans – CHUMA
  • Mtedza wa CG7 / Groundnuts – CG7
  • Soya – TIKOLORE / Soyabeans – TIKOLORE
  • Khobwe / Cowpeas

Mbeu zonsezi ikupezekanso pa mtengo wabwino komanso ndi koponi posaonjezapo ndalama / All seed available against presentation of FISP coupon. No top-up

20181005_060746

Create a free website or blog at WordPress.com.

Up ↑