In preparation for the next planting season Demeter Seed is participating in ag-shows nationwide. This in order to connect with local farmers and inform them on the importance of good seed.
Because it starts with the seed. If the wrong seed is planted all the other inputs and efforts are wasted. If the genetic potential is not there, the optimum utilsation of inputs will not be possible.
Here some impressions.
MH26 FOR DEMETER COMPANY LIMITED.
.a variety for drought torelant seed.
.160 bags /ha
. medium maturity 90 to 100 days.
Dowe otsekemera.
Malangizo kwa alimi a mzanga:
Kumbukirani kudzala /kubyala mbeu in a iliyonse ndi mvula yoyamba.
.CG11,7,10,9
.MH 26,ZM309,ZM523
.SOYA TIKOLORE
.CHUMA, BEANS
.KHOLOPHETHE
Mbeu zonsezi dzalani ndi mvula yoyamba,kuti mukolore zochuluka.
LUNGU AGRODEALER S IKUKUFUNIRANI ZABWINO ZONSE ALIMI CHAKA CHINO CHA 2019 _2020 GROWING SEASON.
LikeLike
MALANGIZO KWA ALIMI
Pamene tikudzala mtedza,CG7,8,9,10,ndi 11,
Tisaiwale kugwilitsa ntchito innocurant was mtedza.innocurant amathandizira kuchulukitsa zokolora zanu alimi.
Dziwani kuti mbeu iliyonse imafuna chakudya mnthaka,ndiye innocurant amathandizira kupereka chakudya ku mbeu zimenezi za Demeter seed.
LikeLike